Mphunzitsi wa timu yaikulu ya dziko lino ya Flames, Patrick Mabedi, wati timu yake yagonja ndi timu ya Burundi kaamba kakuti siinakonzekere bwino. Flames coach: Patrick ‘General’ Mabedi Mabedi wati ...
Bungwe lomenyera Ufulu wa anthu omwe ali ndi ulumali wosiyanasiyana la CHRR mongwirizana ndi bungwe loyang’anira mabungwe ena pa nkhaniyi, la MACODA likuchititsa mkumano wounikira anthuwa pa ufulu ...